Masiku ndi Yesu
Tikupempherera kuti masiku ndi yesu akupatsani mwayi woona za mtima wake ndi m’mene afunira kuti mukhalire mutsogolere ndi kulimbikitsa ena. Tipiliza kupempemphera limodzi pamene pamene mukuyesetsa kupeleka moyo wanu, ubale wanu ndi utumiki wanu moganizilana ndi cholinga cha ufumu. Zikomo poyendera limodzi ndi yesu gulu la mentorlink.
Tsiku 1: Chiyambi Genesis 1:1-26:5; Yesaya 52:7-53:12
Tsiku 2: Kubadwa kodabwitsa Luka 1:3-2:18
Tsiku 3: Ubatizo wa Yesu Luka 3:1-23
Tsiku 4: Satana akumuyesa Yesu Luka 4:1-13
Tsiku 5: Utumiki wa yesu Luka 4:16-31
Tsiku 6: Kudzichepetsa kweni kweni Luka 18:10-14
Tsiku 7: Kugwira modabwitsa Luka 5:4-11
Tsiku 8: Kuukitsa akufa Luka 8:41-56
Tsiku 9: Kusankha khumi ndi awiri Luka 5:27-28, 6:12-16
Tsiku 10: Madalitso Luka 6:17-23
Tsiku 11: Uthenga wa pa phiri (part1) Luka 6:24-42
Tsiku 12: Uthenga wa pa phiri (part 2) Luka 6:24-42
Tsiku 13: Kukhululukidwa ndi kudzudzulidwa Luka 7:36-50
Tsiku 14: Ophunziraakazi Luka 8:1-3
Tsiku 15: Mafunso a Yohane Luka 3:19-20;7:18-23
Tsiku 16: Fanizo la dothi Luka 8:4-15
Tsiku 17: Fanizo la nyali Luka 8:16-21
Tsiku 18: Mphepo ya mkuntho Luka 8:22-26
Tsiku 19: Mizimu yoipa Luka 8:27-39
Tsiku 20: Kudyetsa 5,000 Luka 9:11-17
Tsiku 21: Umwini wa yesu Luka 9:18, 22 28-36
Tsiku 22: Pemphero la ambuye Luka 11:1-4
Tsiku 23: Pemphero ndi nkhawa Luka 11:9-13, 12:22-28; 17:6
Tsiku 24: Anthu aufumu Luka 5:30-32; 17:1-2; 13:18-19
Tsiku 25: Kusemphana pa zaufumu Luka 12:32-34; 13:10-17
Tsiku 26: Msamaria wabwino Luka 10:25-37
Tsiku 27: Bambo osaona Luka 18:35-43
Tsiku 28: Zakeyu Luka 19:1-10
Tsiku 29: Kulowa mogonjetsa Luka 18:31-34; 19:28-41
Tsiku 30: Za ndalama Luka 19:45-48; 21:1-4
Tsiku 31: Ulamuliro wa Yesu Luka 20:1-26
Tsiku 32: Mgonero womaliza Luka 22:7-23
Tsiku 33: Chipinda cha pamwamba Luka 22:26-38
Tsiku 34: Kugulitsidwa Luka 22:40-65
Tsiku 35: Kufunsidwa Luka 22:63-23:11
Tsiku 36: Kupachikida Luka 23:26-38
Tsiku 37: Imfa ya Yesu Luka 23:39-59
Tsiku 38: Wauka Luka 23:56-24:50
Tsiku 39: Kuitanidwa Aroma 3:23, 5:8, 6:23
Tsiku 40: Lamulo lalikulu Mateyu 28:18-20